Machitidwe 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano pamene iwo anamva zimenezi, anangovomereza,+ ndipo anatamanda Mulungu+ kuti: “Chabwino, pamenepa ndiye kuti Mulungu wapereka mwayi kwa anthu a mitundu ina kuti iwonso alape ndi kudzapeza moyo.”+ 1 Akorinto 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 pakuti khomo lalikulu la mwayi wautumiki landitsegukira,+ koma pali otsutsa ambiri.
18 Tsopano pamene iwo anamva zimenezi, anangovomereza,+ ndipo anatamanda Mulungu+ kuti: “Chabwino, pamenepa ndiye kuti Mulungu wapereka mwayi kwa anthu a mitundu ina kuti iwonso alape ndi kudzapeza moyo.”+