Yoweli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+ pakuti m’phiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ monga mmene Yehova ananenera. Amenewa ndi anthu amene Yehova akuwaitana.”+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti “aliyense amene adzaitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+
32 Ndiyeno aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+ pakuti m’phiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ monga mmene Yehova ananenera. Amenewa ndi anthu amene Yehova akuwaitana.”+