Machitidwe 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka ndi kuyenda malo osiyanasiyana m’chigawo cha Galatiya+ ndi Fulugiya,+ ndipo anali kulimbikitsa+ ophunzira onse. Agalatiya 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mukudziwa kuti nthawi yoyamba imene ndinalengeza uthenga wabwino kwa inu chifukwa chakuti ndinali kudwala,+
23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka ndi kuyenda malo osiyanasiyana m’chigawo cha Galatiya+ ndi Fulugiya,+ ndipo anali kulimbikitsa+ ophunzira onse.
13 Koma mukudziwa kuti nthawi yoyamba imene ndinalengeza uthenga wabwino kwa inu chifukwa chakuti ndinali kudwala,+