2 Akorinto 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nditafika ku Torowa+ kukalengeza uthenga wabwino wonena za Khristu, ndipo mwayi wina utanditsegukira mu ntchito ya Ambuye,+ 2 Timoteyo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Unditengerekonso chovala champhepo chimene ndinachisiya ku Torowa+ kwa Karipo ndi mipukutu, makamaka yazikopa ija.
12 Nditafika ku Torowa+ kukalengeza uthenga wabwino wonena za Khristu, ndipo mwayi wina utanditsegukira mu ntchito ya Ambuye,+
13 Unditengerekonso chovala champhepo chimene ndinachisiya ku Torowa+ kwa Karipo ndi mipukutu, makamaka yazikopa ija.