Luka 24:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pamenepo anatseguliratu maganizo awo kuti amvetse tanthauzo la Malemba.+ 1 Akorinto 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero wobzala+ kapena wothirira sali kanthu, koma Mulungu amene amakulitsa.+