Machitidwe 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mu ola lomwelo la usiku, anawatenga ndi kuwatsuka zilonda zawo. Ndipo onse, iye ndi a m’banja lake, anabatizidwa+ mosataya nthawi. Machitidwe 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhala wokhulupirira mwa Ambuye, pamodzi ndi onse a m’banja lake. Ndipo Akorinto ambiri amene anamva uthenga wabwino anayamba kukhulupirira ndi kubatizidwa.
33 Mu ola lomwelo la usiku, anawatenga ndi kuwatsuka zilonda zawo. Ndipo onse, iye ndi a m’banja lake, anabatizidwa+ mosataya nthawi.
8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhala wokhulupirira mwa Ambuye, pamodzi ndi onse a m’banja lake. Ndipo Akorinto ambiri amene anamva uthenga wabwino anayamba kukhulupirira ndi kubatizidwa.