Mateyu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo Yesu anadzudzula chiwandacho, ndipo chinatuluka.+ Nthawi yomweyo mnyamatayo anachira.+