Machitidwe 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Demetiriyo anasonkhanitsa amisiriwo, limodzi ndi anthu ogwira ntchito yokhudzana ndi zinthu zimenezo.+ Ndiyeno anawauza kuti: “Amuna inu, mukudziwa bwino kuti chuma chathu chimachokera m’ntchito imeneyi.+
25 Choncho Demetiriyo anasonkhanitsa amisiriwo, limodzi ndi anthu ogwira ntchito yokhudzana ndi zinthu zimenezo.+ Ndiyeno anawauza kuti: “Amuna inu, mukudziwa bwino kuti chuma chathu chimachokera m’ntchito imeneyi.+