1 Mafumu 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+ Machitidwe 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atalephera kuwapeza, anakokera Yasoni ndi abale ena kwa olamulira a mzindawo, akufuula kuti: “Anthu awa amene abweretsa mavuto+ padziko lapansi kumene kuli anthu, tsopano akupezekanso kuno,
17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+
6 Atalephera kuwapeza, anakokera Yasoni ndi abale ena kwa olamulira a mzindawo, akufuula kuti: “Anthu awa amene abweretsa mavuto+ padziko lapansi kumene kuli anthu, tsopano akupezekanso kuno,