Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+ Machitidwe 13:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo mu salimo lina akunenanso kuti, ‘Simudzalola kuti thupi la wokhulupirika wanu livunde.’+