Luka 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ine ndakupempherera+ iwe kuti chikhulupiriro chako chisathe. Chotero iwenso, ukabwerera, ukalimbikitse+ abale ako.” 2 Akorinto 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amenenso amatitonthoza m’masautso athu onse,+ kuti tithe kutonthoza+ amene ali m’masautso amtundu uliwonse, chifukwa nafenso tatonthozedwa ndi Mulungu.+
32 Koma ine ndakupempherera+ iwe kuti chikhulupiriro chako chisathe. Chotero iwenso, ukabwerera, ukalimbikitse+ abale ako.”
4 amenenso amatitonthoza m’masautso athu onse,+ kuti tithe kutonthoza+ amene ali m’masautso amtundu uliwonse, chifukwa nafenso tatonthozedwa ndi Mulungu.+