Machitidwe 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho onse anafika ku Efeso, ndipo anzakewo anawasiya kumeneko. Koma iye yekha analowa m’sunagoge+ ndi kuyamba kukambirana ndi Ayuda.
19 Choncho onse anafika ku Efeso, ndipo anzakewo anawasiya kumeneko. Koma iye yekha analowa m’sunagoge+ ndi kuyamba kukambirana ndi Ayuda.