Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+ Luka 24:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Kenako anawauza kuti: “Mmene zachitikiramu ndi mmene zinalembedwera kuti Khristu adzazunzika ndi kuuka kwa akufa tsiku lachitatu,+
46 Kenako anawauza kuti: “Mmene zachitikiramu ndi mmene zinalembedwera kuti Khristu adzazunzika ndi kuuka kwa akufa tsiku lachitatu,+