Luka 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+ Yohane 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa chifukwa chimenechi Pilato anayesetsabe kufunafuna njira kuti amumasule. Koma Ayudawo anafuula kuti: “Mukamumasula ameneyu, ndiye kuti si inu bwenzi la Kaisara. Munthu aliyense wodziyesa yekha mfumu, ameneyo ndi wotsutsana ndi Kaisara.”+
2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+
12 Pa chifukwa chimenechi Pilato anayesetsabe kufunafuna njira kuti amumasule. Koma Ayudawo anafuula kuti: “Mukamumasula ameneyu, ndiye kuti si inu bwenzi la Kaisara. Munthu aliyense wodziyesa yekha mfumu, ameneyo ndi wotsutsana ndi Kaisara.”+