Machitidwe 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene Paulo anali kuwayembekezera ku Atene, mtima unamuwawa kwambiri+ poona kuti mumzindawo mwadzaza mafano.
16 Pamene Paulo anali kuwayembekezera ku Atene, mtima unamuwawa kwambiri+ poona kuti mumzindawo mwadzaza mafano.