Machitidwe 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho anamugwira n’kupita naye kubwalo la Areopagi, ndi kunena kuti: “Kodi tingadziweko za chiphunzitso chatsopanochi+ chimene iwe ukuphunzitsa?
19 Choncho anamugwira n’kupita naye kubwalo la Areopagi, ndi kunena kuti: “Kodi tingadziweko za chiphunzitso chatsopanochi+ chimene iwe ukuphunzitsa?