15 Koma sindinagwiritse ntchito dongosolo lililonse loterolo.+ Ndiponso, sikuti ndalemba zimenezi kuti dongosolo limeneli liyambe kugwira ntchito kwa ine ayi, pakuti zingakhale bwino kuti ineyo ndife kusiyana ndi kuti . . . ndipo palibe munthu angatsutse chifukwa chimene ndikudzitamira!+