Yohane 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+ Machitidwe 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene iye anali pa msonkhano limodzi ndi ophunzirawo, anawapatsa malangizo akuti: “Musatuluke mu Yerusalemu,+ koma muyembekezere chimene Atate analonjeza,+ chimene munamva kwa ine.
26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+
4 Pamene iye anali pa msonkhano limodzi ndi ophunzirawo, anawapatsa malangizo akuti: “Musatuluke mu Yerusalemu,+ koma muyembekezere chimene Atate analonjeza,+ chimene munamva kwa ine.