Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+

      Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+

  • Machitidwe 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+

  • Machitidwe 13:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Uthengawo ndi wakuti Mulungu wakwaniritsa lonjezo lonselo kwa ife ana awo mwa kuukitsa Yesu.+ Zimenezi n’zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mu salimo lachiwiri kuti, ‘Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala Atate wako.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena