Yesaya 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye adzasangalala ndi kuopa Yehova.+ Sadzaweruza potengera zimene wangoona ndi maso ake, kapena kudzudzula potengera zimene wangomva ndi makutu ake.+ 2 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chiweruzo cha Mulunguchi n’cholungama chifukwa akubwezera masautso kwa amene amakusautsani.+
3 Iye adzasangalala ndi kuopa Yehova.+ Sadzaweruza potengera zimene wangoona ndi maso ake, kapena kudzudzula potengera zimene wangomva ndi makutu ake.+