1 Timoteyo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona,+ sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndikhale mphunzitsi wophunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro+ ndi choonadi. 2 Timoteyo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uthenga wabwino umenewu ndi umene anandiikira kuti ndikhale mlaliki, mtumwi ndi mphunzitsi.+
7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona,+ sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndikhale mphunzitsi wophunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro+ ndi choonadi.