Yohane 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Lekani kuweruza poona maonekedwe akunja, koma muziweruza ndi chiweruzo cholungama.”+ 1 Akorinto 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mdulidwe+ sutanthauza kalikonse, ndipo kusadulidwa+ sikutanthauza kanthu, koma kusunga malamulo a Mulungu ndiko kofunika.+
19 Mdulidwe+ sutanthauza kalikonse, ndipo kusadulidwa+ sikutanthauza kanthu, koma kusunga malamulo a Mulungu ndiko kofunika.+