Yohane 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu mumalambira chimene simuchidziwa.+ Ife timalambira chimene tikuchidziwa, chifukwa chipulumutso chikuchokera kwa Ayuda.+
22 Inu mumalambira chimene simuchidziwa.+ Ife timalambira chimene tikuchidziwa, chifukwa chipulumutso chikuchokera kwa Ayuda.+