2 Akorinto 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu akhale mboni+ pa moyo wanga kuti chifukwa chimene sindinabwererebe ku Korintoko n’chakuti sindinafune kuti ndidzawonjezere chisoni chanu.+ Afilipi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu ndiye mboni yanga kuti ndikufunitsitsa nditakuonani nonsenu. Ndikufunitsitsa nditakuonani ndi chikondi chachikulu+ ngati chimene Khristu Yesu ali nacho.
23 Mulungu akhale mboni+ pa moyo wanga kuti chifukwa chimene sindinabwererebe ku Korintoko n’chakuti sindinafune kuti ndidzawonjezere chisoni chanu.+
8 Mulungu ndiye mboni yanga kuti ndikufunitsitsa nditakuonani nonsenu. Ndikufunitsitsa nditakuonani ndi chikondi chachikulu+ ngati chimene Khristu Yesu ali nacho.