Salimo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+ Yakobo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti lilime timatamanda nalo Yehova,+ amenenso ndi Atate,+ komanso ndi lilime lomwelo timatemberera+ anthu amene analengedwa “m’chifaniziro cha Mulungu.”+
7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+
9 Pakuti lilime timatamanda nalo Yehova,+ amenenso ndi Atate,+ komanso ndi lilime lomwelo timatemberera+ anthu amene analengedwa “m’chifaniziro cha Mulungu.”+