12 Mwachitsanzo, onse amene anachimwa popanda chilamulo adzawonongekanso popanda chilamulo.+ Koma onse amene anachimwa ali ndi chilamulo+ adzaweruzidwa ndi chilamulo.+
10 Pakuti onse odalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Ndi wotembereredwa aliyense wosapitiriza kuyenda m’zinthu zonse zolembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi kuzichita.”+