1 Atesalonika 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso usiku ndi usana timapereka mapembedzero amphamvu+ kuti tidzaone nkhope zanu ndi kukwaniritsa zimene zikusowa pa chikhulupiriro chanu.+ 2 Timoteyo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikuyamika Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika+ monga mmene makolo anga+ anachitira, ndipo ndikuuchita ndi chikumbumtima choyera.+ Ndikumuyamika chifukwa chakuti sindiiwala za iwe m’mapembedzero anga,+ usana ndi usiku,
10 Komanso usiku ndi usana timapereka mapembedzero amphamvu+ kuti tidzaone nkhope zanu ndi kukwaniritsa zimene zikusowa pa chikhulupiriro chanu.+
3 Ndikuyamika Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika+ monga mmene makolo anga+ anachitira, ndipo ndikuuchita ndi chikumbumtima choyera.+ Ndikumuyamika chifukwa chakuti sindiiwala za iwe m’mapembedzero anga,+ usana ndi usiku,