Afilipi 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero, ngati pakati panu pali kulimbikitsana kulikonse mwa Khristu,+ kaya kutonthozana kulikonse kwa chikondi, kaya mzimu woganizirana,+ kaya chikondi chachikulu+ chilichonse ndi chifundo, 1 Atesalonika 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho pitirizani kutonthozana ndi kulimbikitsana+ monga mmene mukuchitira.+ Aheberi 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tisaleke kusonkhana pamodzi,+ monga mmene ena achizolowezi chosafika pamisonkhano akuchitira. Koma tiyeni tilimbikitsane,+ ndipo tiwonjezere kuchita zimenezi, makamaka pamene mukuona kuti tsikulo likuyandikira.+
2 Chotero, ngati pakati panu pali kulimbikitsana kulikonse mwa Khristu,+ kaya kutonthozana kulikonse kwa chikondi, kaya mzimu woganizirana,+ kaya chikondi chachikulu+ chilichonse ndi chifundo,
25 Tisaleke kusonkhana pamodzi,+ monga mmene ena achizolowezi chosafika pamisonkhano akuchitira. Koma tiyeni tilimbikitsane,+ ndipo tiwonjezere kuchita zimenezi, makamaka pamene mukuona kuti tsikulo likuyandikira.+