Salimo 85:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwakhululukira anthu anu zolakwa zawo.+Mwaphimba machimo awo onse.+ [Seʹlah.] Yesaya 43:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ineyo ndi amene ndikufafaniza+ zolakwa zako,+ ndipo machimo ako sindidzawakumbukiranso.+