Salimo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Wodala ndi munthu amene wakhululukidwa zolakwa zake, amene machimo ake aphimbidwa.+