Agalatiya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti ngati cholowa chimene Mulungu amapereka chimadzera m’chilamulo, ndiye kuti sichidaliranso lonjezo,+ koma Mulungu mokoma mtima wachipereka kwa Abulahamu mwa lonjezo.+
18 Pakuti ngati cholowa chimene Mulungu amapereka chimadzera m’chilamulo, ndiye kuti sichidaliranso lonjezo,+ koma Mulungu mokoma mtima wachipereka kwa Abulahamu mwa lonjezo.+