Genesis 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzakupatsa ana ambiri zedi, ndipo mwa iwe mudzatuluka mitundu ndi mafumu.+