Yohane 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu simunandisankhe ine, koma ine ndinakusankhani. Ndinakuikani kuti mupitirize kubala zipatso zochuluka,+ ndi kutinso zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate m’dzina langa akupatseni.+ Afilipi 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Si kuti mtima wanga uli pa mphatsoyo ayi,+ koma ndikufunitsitsa kuti mulandire madalitso+ amene adzawonjezere phindu pa zimene muli nazo.
16 Inu simunandisankhe ine, koma ine ndinakusankhani. Ndinakuikani kuti mupitirize kubala zipatso zochuluka,+ ndi kutinso zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate m’dzina langa akupatseni.+
17 Si kuti mtima wanga uli pa mphatsoyo ayi,+ koma ndikufunitsitsa kuti mulandire madalitso+ amene adzawonjezere phindu pa zimene muli nazo.