Hoseya 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene iwo achuluka, m’pamenenso akundichimwira kwambiri.+ M’malo mondipatsa ulemu, akundinyoza.+ Hoseya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo, mofanana ndi munthu wochokera kufumbi, aphwanya pangano.+ Andichitira zachinyengo kumalo kumene amakhala.+
7 Koma iwo, mofanana ndi munthu wochokera kufumbi, aphwanya pangano.+ Andichitira zachinyengo kumalo kumene amakhala.+