1 Akorinto 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi. Agalatiya 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti nonsenu amene munabatizidwa mwa Khristu+ mwavala Khristu.+
13 Pakuti ndi mzimu umodzi, tonsefe tinabatizidwa+ kukhala thupi limodzi, kaya tikhale Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena mfulu, ndipo tonsefe tinamwetsedwa+ mzimu umodzi.