Salimo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+
19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+