Yohane 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzadziwa choonadi,+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ Aheberi 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akuchititsa anthu amene akuyeretsedwa kukhala angwiro kwamuyaya,+ kudzera mu nsembe imodzi yokha basi.+
14 Iye akuchititsa anthu amene akuyeretsedwa kukhala angwiro kwamuyaya,+ kudzera mu nsembe imodzi yokha basi.+