Aroma 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi pa nthawiyo munali kukhala ndi zipatso zotani?+ Zinali zinthu+ zimene tsopano mumachita nazo manyazi. Ndipo pothera pake pa zinthu zimenezo ndi imfa.+ Aheberi 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuli bwanji magazi+ a Khristu, amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu wamuyaya?+ Kodi magazi amenewo sadzayeretsa+ zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika+ kwa Mulungu wamoyo?
21 Kodi pa nthawiyo munali kukhala ndi zipatso zotani?+ Zinali zinthu+ zimene tsopano mumachita nazo manyazi. Ndipo pothera pake pa zinthu zimenezo ndi imfa.+
14 kuli bwanji magazi+ a Khristu, amene anadzipereka wopanda chilema kwa Mulungu kudzera mwa mzimu wamuyaya?+ Kodi magazi amenewo sadzayeretsa+ zikumbumtima zathu ku ntchito zakufa,+ kuti tichite utumiki wopatulika+ kwa Mulungu wamoyo?