Yohane 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khalani ogwirizana ndi ine, inenso ndikhala wogwirizana ndi inu.+ Nthambi singabale zipatso payokha, pokhapokha ngati ndi yolumikizikabe kumpesawo. Chimodzimodzi inunso, simungabale zipatso mukapanda kukhala olumikizika kwa ine.+ 1 Yohane 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amene amanena kuti ndi wogwirizana+ naye, ayenera kupitiriza kuyenda mmene iyeyo anayendera.+ 1 Yohane 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense amene ali wogwirizana+ ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Aliyense amene amachita tchimo ndiye kuti sanamuone kapena kumudziwa.+
4 Khalani ogwirizana ndi ine, inenso ndikhala wogwirizana ndi inu.+ Nthambi singabale zipatso payokha, pokhapokha ngati ndi yolumikizikabe kumpesawo. Chimodzimodzi inunso, simungabale zipatso mukapanda kukhala olumikizika kwa ine.+
6 Aliyense amene ali wogwirizana+ ndi Yesu sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo.+ Aliyense amene amachita tchimo ndiye kuti sanamuone kapena kumudziwa.+