Luka 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu anali kupemphera pamalo enaake. Atatsiriza, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Ambuye, tiphunzitseni kupemphera,+ ngati mmene Yohane anaphunzitsira ophunzira ake.”+
11 Tsopano Yesu anali kupemphera pamalo enaake. Atatsiriza, mmodzi wa ophunzira ake anamuuza kuti: “Ambuye, tiphunzitseni kupemphera,+ ngati mmene Yohane anaphunzitsira ophunzira ake.”+