Mateyu 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mofanana ndi zimenezi inunso, pamaso pa anthu, mumaonekadi ngati olungama+ koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo. Tito 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Asamasamale nthano zachiyuda+ ndi malamulo a anthu+ amene asiya choonadi.+
28 Mofanana ndi zimenezi inunso, pamaso pa anthu, mumaonekadi ngati olungama+ koma mkati mwanu mwadzaza chinyengo ndi kusamvera malamulo.