2 Akorinto 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Timazunzidwa, koma osati mochita kusowa kolowera.+ Timagwetsedwa pansi,+ koma sitiwonongedwa.+