Luka 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komano zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima woona+ komanso wabwino, amawagwiritsitsa ndi kubereka zipatso mwa kupirira.+ 2 Akorinto 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+
15 Komano zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima woona+ komanso wabwino, amawagwiritsitsa ndi kubereka zipatso mwa kupirira.+
19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+