Salimo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zingwe zawo zoyezera zafika padziko lonse lapansi,+Mawu awo amveka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.+Kumwambako Mulungu wamangira dzuwa hema.+
4 Zingwe zawo zoyezera zafika padziko lonse lapansi,+Mawu awo amveka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.+Kumwambako Mulungu wamangira dzuwa hema.+