Mateyu 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa, ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina, ndipo musalowe mumzinda wa Asamariya.+ Machitidwe 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Anthu inu a m’Yudeya ndi inu nonse okhala m’Yerusalemu,+ dziwani ndi kutchera khutu ku zimene ndikufuna kukuuzani pano.
5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa, ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina, ndipo musalowe mumzinda wa Asamariya.+
14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Anthu inu a m’Yudeya ndi inu nonse okhala m’Yerusalemu,+ dziwani ndi kutchera khutu ku zimene ndikufuna kukuuzani pano.