Aroma 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo musapereke ziwalo zanu ku uchimo+ kuti zikhale zida zochitira zinthu zosalungama,+ koma dziperekeni kwa Mulungu monga anthu amene auka kwa akufa.+ Ziwalo zanunso muzipereke kwa Mulungu monga zida+ zochitira chilungamo.
13 Ndipo musapereke ziwalo zanu ku uchimo+ kuti zikhale zida zochitira zinthu zosalungama,+ koma dziperekeni kwa Mulungu monga anthu amene auka kwa akufa.+ Ziwalo zanunso muzipereke kwa Mulungu monga zida+ zochitira chilungamo.