Tito 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mofanana ndi zimenezi, pitiriza kulimbikitsa anyamata kuti akhale oganiza bwino.+ 1 Petulo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira.+ Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+
7 Koma mapeto a zinthu zonse ayandikira.+ Choncho khalani oganiza bwino,+ ndipo khalani maso kuti musanyalanyaze kupemphera.+