1 Akorinto 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano mphatso zilipo zamitundumitundu,+ koma mzimu ndi umodzi,+ Aefeso 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinakhala mtumiki+ wa zimenezi mogwirizana ndi mphatso yaulere ya kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene ndinapatsidwa mogwirizana ndi mmene mphamvu yake imagwirira ntchito.+
7 Ndinakhala mtumiki+ wa zimenezi mogwirizana ndi mphatso yaulere ya kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene ndinapatsidwa mogwirizana ndi mmene mphamvu yake imagwirira ntchito.+