1 Atesalonika 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani+ mwa Ambuye ndi kukulangizani. 1 Petulo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wetani+ gulu la nkhosa za Mulungu+ lomwe analisiya m’manja mwanu, osati mokakamizika, koma mofunitsitsa.+ Osatinso chifukwa chofuna kupindulapo kenakake,+ koma ndi mtima wonse.
12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani+ mwa Ambuye ndi kukulangizani.
2 Wetani+ gulu la nkhosa za Mulungu+ lomwe analisiya m’manja mwanu, osati mokakamizika, koma mofunitsitsa.+ Osatinso chifukwa chofuna kupindulapo kenakake,+ koma ndi mtima wonse.