Aroma 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo ndipo munakhala akapolo a Mulungu,+ mukukhala ndi zipatso+ za chiyero, ndipo pa mapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+
22 Koma tsopano chifukwa munamasulidwa ku uchimo ndipo munakhala akapolo a Mulungu,+ mukukhala ndi zipatso+ za chiyero, ndipo pa mapeto pake mudzakhala ndi moyo wosatha.+